Anthu ochita ziwonetsero ati a Chakwera atule pansi udindo
Anthu okhudzidwa omwe akudana ndikukwera kwa mitengo ya zinthu mumzinda wa Blantyre ati apempha mtsogoleri wa dziko lino Dr. Lazarus Chakwera kuti atule pansi udindo wawo kamba kolephera kusintha dziko…