NDIKUFUNA NANKHUMWA AZIMUGWADIRA MUTHARIKA-Namalomba
Mneneri wa Chipani cha DPP a Shadreck Namalomba,awunza Kondwani Nankhumwa kuti asamapange ziganizo payekha akafuna kuchita zinthu. A Namalomba ati,Nankhumwa akamafuna kuchita chinthu chokhuzana ndi mu chipani cha DPP, aziyamba amufusa kale…
Read More




