Amalawi Akufuna Kafukufuku wa Ngozi ya Ndege ya a Chilima Ufale Live pa Radio
By Suleman Chitera Anthu ambiri ku Malawi akupitiriza kufuna kuti kafukufuku wokhudza ngozi ya ndege yomwe inapha Vice President Saulos Klaus Chilima uchitike momveka bwino komanso poyera, kuphatikizapo kufalitsidwa live…







