Lipipa Amanga Chipatala Cha Manase

Ichi ndi chipatala cha Manase chomwe akumanga ndi Phungu wa Blantyre City South wolemekezeka a Noel Lipipa.

Kubwera kwa a Noel Lipipa ku dera la Blantyre City South zinthu zambiri zikuchitika ndipo zitukuko ndie ndi mbwee.

Anthu aku derali ayamikira a Lipipa kamba kogwiritsa ntchito Constituency Development Fund (CDF) moyenerera.

Noel Lipipa kusintha Blantyre City south!

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *