Kampani yopanga sugar ya Illovo Sugar Malawi plc yakweza mtengo wa sugar kuyambira lero.
Mwachitsanzo, kampaniyi yati paketi ya shuga yolemera 1 kg tsopano adzigulitsidwa pa K2 300 kuchoka pa K2 000.
Kukwera mtengoku kwadza ngakhale aMalawi ambiri akulephera kupeza sugar pa msika, zomwe zapangitsa kut ogulitsa malonda nawo akweze mtengo kufika pa K3 500 pa pakeyi yomweyi.
Ekhaya Holiday Resort fully open