Zimafunika Kukhalako Okula Mtima Pang’ono kuti zina ziyende-Mabedi
Mphunzitsi wa timu ya Malawi Patrick Mabedi wati ngati mphunzitsi pena zimayenera kuoneka ngati wamwano kuti zinthu zina ziyende. Iye amayankhula izi poyankha mafunso kwa atolankhani pakutha pa masewero omwe…









