Zifukwa Zomwe Tikufunira Bright Msaka Adzatitsogolere
KUTHETSA KATANGALEAdzakweza malipiro a anthu ogwira ntchito m’boma ndicholinga choti munthu azidzakwaniritsidwa ndi malipiro ake ndipo asadzakhale ndichilakololako chosokoneza chuma chaboma.Adzakhazikitsa malamulo okhwima opereka chilango kwa anthu omwe asokoneza chuma chadziko lino kuti ena adzatengere phunziro. KUTUKULA CHUMAAdzakhazikitsa ndondomeko yoyenera yobwezeretsa chuma chadziko lino mchimake komanso adzaika njira zotetezera chuma chadziko lino kuti chisamadzaonongeke mukatangale […]
