1 min read

Chakwera’s Administration No Solution To The Current Economic Challenges

Consumers Association of Malawi (CAMA) claims PresidentLazarus Chakwera’s led administration has no capacity to solve current socio-economic challenges that have rocked the country. Its Executive Director, John Kapito says the president himself does not live by his words. “The President comes from a background where his entire life he promised people heaven and none held […]

1 min read

Chakwera Akudabwisa Poikira Kumbuyo Buluma, Kachaje

Boma la President Lazarus Chakwera laimbidwa mlandu chifukwa chophwanya lamulo la Ombudsman lochotsa mkulu wa bungwe la Malawi Energy Regulatory Authority (MERA) Henry Kachaje ndi wachiwiri kwa mkulu wa National Oil Company (Nocma) Helen Buluma paudindo wawo. Ombudsman Grace Malera adathetsa kusankhidwa kwa Kachaje mu Novembala chatha atapeza kuti analibe digiri ya master yomwe amafunikira […]

1 min read

Kukanirana Kwabuka Pa Ndalama Zomwe Zinaonongedwa Ku UNGA

Akuluakulu m’boma akukanirana komanso kukankhirana zokhudza lipoti la ndalama zomwe zidagwira ntchito ku mkumano wa United Nations General Assembly m’dziko la America komwe President Lazarus Chakwera ndi anthu ena 37 adapita. Pafupifupi mwezi watha tsopano President Chakwera atabwera ku ulendowu koma nduna zake zikuchita jenkha kupereka lipoti za momwe misonkho ya aMalawi idagwilira ntchito. Poyambilira, […]

1 min read

Government to increase internet access to 80 percent by 2026

Lilongwe, November 2: Minister of Information and Digitalisation, Gospel Kazako has announced that government intends to increase internet access to 80 percent by 2026. The Minister disclosed this during a press briefing on digitalisation developments in Lilongwe. Kazako said government has also partnered with Starlink which is a low cost internet broadband to help in […]