Civil Service United ndi MAFCO FC alepherana posagoletsana
Ma timu a Civil Service United ndi MAFCO FC alepherana posagoletsana chigoli chili chonse ngati zopangana pamasewero omwe analipo masanawa pa bwalo la Civo mu ligi ya TNM. Poyankhula atatha masewerowa, wachiwiri kwa mphunzitsi ku Civil, Wilson Chidati, wamvomereza kuti mpira unawavuta kamba koti chili chonse chomwe anakonzekera sichinatheke pamasewerowa. Read moreFAM announces Airtel Top […]