Ichi ndi chigoli cha namba18 mu ligi ya mpira wamiyendo wa azimayi ku France.
Iye anamwetsa chigoli choyamba mu mphindi 30 pa masewero amene timu yake ya PSG yafanana mphamvu 3-3 ndi timu ya Guingamp.
News from Malawi you can trust