Sindingalowe UTM yomwe ili ndi aphungu anayi – Nankhumwa
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha Democratic Progressive Party (DPP) kumwera Kondwani Nankhumwa wanena mphekesera zoti akufuna kugulitsa chipanichi ku UTM kapena Malawi Congress Party (MCP). A Nankhumwa amalankhula izi…









