Mlembi wamkulu wa chipani cha PP Mr Chikhame wati chimanga chomwe boma la Malawi likugawa chabwera chifukwa Cha mtsogoleri wa chipani cha PP Dr Joyce Banda.
Iwo ati chimangachi chinachokela ku dziko la Ukraine chifukwa champando omwe mtsogoleri wawo anapasidwa ndi mtsogoleri wa Ukraine ngati Ambassador.
Read also: Why do Africans do this to other Africans?”
Read also: President’s Convoy Attacked in Chikwawa, Malawi, Sparking Widespread Condemnation
Read also: 888bet appoints Phyzix as brand ambassador in Malawi
Iwo achenjedza chipani Cha MCP kuti chileke kugwiritsa ntchito chimanga Cha Ukraine ngati campaign chifukwa chinabwera kuno pansi pautsogoleri wa mayi Dr Joyce Banda.
Iwo aonjezelatso kuti chipani cha PP chizayima pa choka mchisankho Cha mawa. Iwo ati a Banda akhala akulangiza boma la a Chakwera koma sakumva malangizo a Dr Banda.
Read also: Will ADMARC Be Called The Granary For Farmers Again?
Read also: PDP Youth Leader Austin Nsopela Backs DPP’s Peter Mutharika Amid Malawi Election Lead
Read also: MACRA FM Spectrum re-framing to address broadcasting challenges





