Chipani Cha DPP Chati Chodabwa Kuti Police Sinamange Wina Aliyense Pa Zipolowe Za Ku Lilongwe

Chipani cha Democratic Progressive Party _ DPP chati chikudabwa kuti mpaka pano a polisi sanamangepo munthu wina aliyese yemwe akukhudzidwa ndi zachipongwe zomwe otsatila chipani cha MCP anapangira otsatila Chipani cha DPP ku Lilongwe pa mbowe filling station.

Nkulu osutsa boma kunyumba ya Malamulo a Mary Navicha, ati akudabwa nazo kuti apolisi akugwiritsidwa ntchito ngati achipani m’malo mogwira ntchito yawo yopeleka chitetezo. Chipongwe Chochitika Lachisanu koma mpaka pano palibe yemwe wanjatidwa. ” Ngati a Chakwera akuzitengela Masewera izi zitha kuzayambitsa Nkhondo m’dziko muno” Anatero a Navicha.

A Navicha anapitilira kunena kuti ” Ngati chipani cha DPP tiliso ndi kuthekera koti tikhoza kukwanitsa zomwe akupanga a MCP ku m’chigawo chapakati chawo chomwe koma ife timakonda Mtendere chifukwa Nkhondo simanga mudzi”.

Iwo amalakhula izi pamene amawona ena mwa ovulazidwa pachiwembucho.

Related Posts

DPP Blues Rebels Brings Division In

The way Charles Mchacha is castigating the Leader of Opposition in Parliament, Hon Kondwani Nankhumwa, is just testimony enough that Read more

Malawi Freedom Network advice President Banda to fight corruption

If you thought Malawians are lazy people, I bet you a Dinosaur, think twice and you will know, check in Read more

David Bisnowaty Israeli-Born Malawi Parliament Member: Actions, Not Words, Will Change Africa for the Better

Malawi MP David Bisnowaty. How does the Israeli-born son of an eastern European Holocaust survivor end up as a parliament Read more

Mustag Chothia, Sulema Ismael Karim In Land scam

Land remains one area that Malawians know has been heavily abused, characterised by ownership wrangles, not to mention corruption, fueled Read more

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

FDH Launch Islamic Banking Window