Chilima akhoza kudikira madzi amphutsi”- atero Dr. Chaima

Katswiri pa nkhani za ndale ndi ulamuliro wabwino mdziko muno a Dr George Chaima alangiza wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Dr Saulos Chilima kuti ayambe kukonzekela zodzayima pa chisankho cha chaka cha mawa ngati mtsogoleri wa chipani cha UTM posatengera za mgwirizano omwe ulipo pakatipa iwo ndi Dr. Lazarus Chakwera.

A Chaima ati a Chilima achedwa akadalira kwambiri mgwirizano wawo omwe anagwirizana pa zisankho za chaka cha 2020.

Malingana ndi a Chaima ati zomwe chapanga chipani cha Malawi Congress, kunena kuti Dr. Chakwera adzayimira ngati mtsogoleri wachipanichi chaka cha mawa sikulakwa kuli konse.

Related Posts

DPP Blues Rebels Brings Division In

The way Charles Mchacha is castigating the Leader of Opposition in Parliament, Hon Kondwani Nankhumwa, is just testimony enough that Read more

Malawi Freedom Network advice President Banda to fight corruption

If you thought Malawians are lazy people, I bet you a Dinosaur, think twice and you will know, check in Read more

David Bisnowaty Israeli-Born Malawi Parliament Member: Actions, Not Words, Will Change Africa for the Better

Malawi MP David Bisnowaty. How does the Israeli-born son of an eastern European Holocaust survivor end up as a parliament Read more

Mustag Chothia, Sulema Ismael Karim In Land scam

Land remains one area that Malawians know has been heavily abused, characterised by ownership wrangles, not to mention corruption, fueled Read more

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

FDH Launch Islamic Banking Window