
Notice: Undefined index: post in /home/kingwpmf/malawifreedomnetwork.com/wp-content/plugins/awesome-ads/awesome-ads.php on line 194
Timu ya Salima Secondary School yamalizira pa nambala yachitatu mu mpikisano wa African Schools Championship kutsatira kugonjetsa timu ya Sainte Rita 3-1
Blessings Sakala, Ishmael Bwanali komanso Latumbikika Kayira ndi omwe anagoletsa kumbali ya Salima Secondary school
Salima secondary school itenga ndalama zokwana $150,000 (pafupifupi K150 milllion) pomaliza pa nambala yachitatu