Asilikali alephera kupherera chipolopolo cha Mapale
Nkhope za ochemelera a FCB Nyasa Big Bullets zikupitilirabe kulemedwa ndichisangalaro pamene timuyi yagonjetsa Moyale Barracks 3-1 mumasemifainolo a FDH Bank Cup pa bwalo la Bingu mu nzinda wa Lilongwe. Chipambanochi chikudza, patangodutsa masiku atatu timu yovala zoyera ndi zofiirayi itagonjetsa Red Arrows ya m’dziko la Zambia 2-1 mumasewero oyamba a CAF Champions League. Chigoli […]
