Tikufuna kusula aphunzitsi kuti azipikisana ndi ena kunja kwa dziko lino – FAM
Football Association of Malawi (FAM) yati khumbo lawo ndilofuna kutulutsa chiwerengero chochuluka cha aphunzitsi a mpira wamiyendo oti azitha kumpikisana ndi aphunzitsi omwe akuchita bwino kunja kwa dziko lino. Wachiwiri kwa mtsogoleri wa FAM, Christopher Madalitso Kuyera, walankhula izi lero, lachinayi, pa 29 August 2024 ku Mpira Village ku Chiwembe mu nzinda wa Blantyre pomwe […]
