Kodi kafukufuku wa ngozi ya ndege yomwe inapha Dr Saulos Chilima zili pati? Amalawi akufunsa APM
By Suleman Chitera Amalawi ambiri akupitiriza kufunsa ndi kudandaula za kusowa kwa zotsatira zomveka pa kafukufuku wa ngozi ya ndege yomwe inapha Saulos Chilima. Nkhaniyi ikubweranso mwamphamvu potsatira lonjezo limene…









