Sun. Apr 28th, 2024

Tili Ku Bagamoyo komwe chilichonse chakwera ndi Chakwera – Mutharika

Mtsogoleri wakale wa dziko lino yemweweso ndi mtsogoleri wachipani chotsutsa boma cha Democratic Progressive -DPP Prof. Peter Munthalika wadzudzura boma la Dr. Lazarus Chakwera ati kamba kolephera kuyendetsa bwino dziko lino.

A Munthalika amalankhura izi masanawa pa msonkhano wa atolankhani omwe umachitikira kunyumba kwawo ku Mangochi.

Iwo ati ndizomvetsa chisoni kuti aMalawi akulephera kupeza zinthu zofunikira monga ziphaso zoyendera (passports)komaso ziphaso zoyendetsera galimoto.

Iwo ati ngakhale mavutowa alipo m’dziko muno aMalawi asadandaule ndipo asadere nkhawa chifukwa chipani chawo chakonzeka kudzamuliraso dziko lino akasankhidwa pa chisankho cha chaka chamawa.

Related Posts

DPP Blues Rebels Brings Division In

DPP Blues Rebels Brings Division In

The way Charles Mchacha is castigating the Leader of Opposition in Parliament, Hon Kondwani Nankhumwa, is just testimony enough that Read more

Malawi business tycoon Simbi Phiri disassociates himself from forming up “Congress for Democrats”

Business Mogul Simbi Ashan Phiri who is Executive Chairman of Katho Civils has disassociated himself from social media rumours that Read more

Navicha appointed as a leader of opposition in parliament

Member of parliament for Thyolo Thava, Mary Thom Navicha has been recently appointed as a new leader of opposition following Read more

Jumah says it is possible to change Malawi in 10-15 years

By Vincent Gunde President and Commander in Chief of Muvi wa Chilungamo Revolutionary Party (MRP) Bantu Saunders Jumah, says it Read more

Other stories

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Ekhaya luxury Resort fully open