Njanjeyo siyawo ndiya Mozambique _ Namalomba
Mneneri wachipani cha Democratic Progressive (DPP) Shadreck Namalomba wati ndiwodabwa kuti mtsogoleri wadziko lino akuwuza mtundu wa a Malawi kuti boma lake labweretsa mafuta agalimoto lachitatu kudzera panjanji. Izi zikudza pomwe mtsogoleri wadziko lino Dr Lazarus Chakwera lachitatu analandila sitima yapanjanji yobweletsa mafuta agalimoto m’boma la Nsanje yomwe akuti patha zaka zoposa 40 isanakuyenda. Read […]