
Nkhani Za Fertilizer Ku Dowa Central East
By Rev. Flywell Somanje.
Read also: High Court Dismisses Namalomba’s Application With Costs
Read also: FAM boss to fly COSAFA flag at CAF
Malinga ndikafuku yemwe wachitika ndi Bungwe la MiRECE, mosemunja yambikira tchito yongawa fertilizer Dziko Muno athu odzungulira Dowa Boma sanapezebe fertilizer mpaka lero, chikuyimitsa mutu athu ndi chakuti apa ndi pa mchombo pa Boma la Dowa, Koma fertilizer akungawidwa kwambiri kumandera komwe ma MP akuchokera, ku Mvera komwe akuchokera MP chimwendo, KU dera la Lumbadzi komwe akuchokera MP DAUD,ku Chibazi konwe akuchokera MP Kawale zikuyendaso, fuso ndikumati athu aku Dowa Central east analakwanji, madadaulo awo achuluka, KU derari palibe chitukuko cholozeka chosecho ma MP atatu onse amathera pamenepa, m’mbuyomu Bungwe lanthu (MIRECE) linapempa kuti MEC idure dera, (consutuency) Tikuthoza MEC kuti zinachika, Koma izi sizikutathauza kuti ma MP atatuwa aleke kugwira tchito KU derari palipano Monga zikukhalilamu, iwompaka 2025 akadzachita masakho! Tikupepha Bungwe la MEC kuti naloso liunikire’ Sibwino kuti Zika Zina zizimanidwa chitukuko Dziko lomwelino! Rev somanje!
Read also: Japanese Embassy hailed for enhancing security and hygiene at Ngwenya Primary School
Read also: Mpikisano wa Airtel Top 8
Read also: Reverend Father Dr. Wilfred Sumani Appointed Acting Vice Chancellor of Catholic University of Malawi


















