Chakaka Nyirenda ali kokasaka komwe ndalama za AIP zidapita Zokwana k30 Billion Zomwe Lowe Anabetsa

Mkulu wa malamulo m’dziko muno Thabo Chakaka Nyirenda ali m’dziko la Germany kusaka ndalama za amerika zokwana 543,000 zomwe zidasowa pomwe boma limafuna kugula feteleza

Chakaka Nyirenda wati ali kumeneko kulondoloza mapepala omwe athandizire pa kupezeka kwa ndalamazi

Boma la Malawi linabetsa ndalama zokwana K 750 million ku kampani ya Barkaat Foods Limited yomwe inkati igulitsa unduna wa zaulimi feteleza otsika mtengo

Lowe anatenga ndalama zokwana k30 Billion kupereka ku barkaat foods kuti agule fertilizer ndipo company ya barkaat foods inasowa ndi ndalamazo

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *