Sindingapepese chifukwa Dambwe ndi malo Amizimu Yakufa, Nanga Ndikapepese ziwanda? – Enock Kanzingeni Chihana
“Sindingawope chifukwa ndimayankhulira aMalawi osauka komanso chipani! Ulamuliro opanda masomphenya omwe ukutsogozedwa ndi mizimu yoyipa ukuyesera kuzunza anthu osalakwa kuti ukachite ufumu pamaso pa amphawi […]
