Uku Ndiye Kukhala-Katswiri Pa Ndale Ayamikira Chakwera

Katswiri pa ndale, Czar Kondowe wayamikira mtsogoleri wa dziko lino Dr.Lazarus Chakwera potumiza wachiwiri wake, Dr Saulos Chilima kukakhala nawo pa mwambo okumbukira umodzi m’dziko la Tanzania.

Kondowe wati izi zikuonetseratu ubale wabwino omwe ulipo pakati pa a Chakwera ndi a Chilima.

Kondowe watiso anthu akhala akuyankhula zosiyana-siyana zokhudza ubale wa anthu awiri-wa ndipo izi zithandizira kuchotsa maganizo olakwika omwe anthu amakhala nawo okhudza ubale wa atsogoleri-wa.

Komabe, Kondowe wapempha a Chakwera kuti asasiyire pompa koma apitilize kumawatuma a Chilima mu ntchito zosiyana-siyana.

Aka ndi koyamba kuchokera m’chaka cha 2022 kuwona mtsogoleri wa dziko lino akutuma a Chilima kuti akawaimire kunja kwa dziko lino.

Related Posts

Malawi Freedom Network advice President Banda to fight corruption

If you thought Malawians are lazy people, I bet you a Dinosaur, think twice and you will know, check in Read more

David Bisnowaty Israeli-Born Malawi Parliament Member: Actions, Not Words, Will Change Africa for the Better

Malawi MP David Bisnowaty. How does the Israeli-born son of an eastern European Holocaust survivor end up as a parliament Read more

Biography Of Zuneth Sattar

Zuneth Sattar Director of Xaviar Limited and Xaviar Investments Limited Zuneth Sattar is an experienced and knowledgeable property investor. With Read more

Zuneth Sattar Is An Experienced Property Investor

PROPERTY INVESTOR PROPERTY MARKET AN OVERVIEW This blog will cover a wide range of topics and subjects that relate to Sattar’s Read more

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

FDH Launch Islamic Banking Window