2025 Dr Saulos Chilima Azapezeka Pa Ballot Paper Ngati Mtsogoleri wa Tonse Alliance

NJAWALA WATI MGWILIZANO WA CHAKWERA NDI CHILIMA UNACHITIKA PAMASO PAKHOTI

Pamene Chipani cha Malawi Congress Party MCP chasakha Dr Lazarus chakwera Ngati yemwe atazawaimilire pachisakho cha 2025. Koma Mlembi ku Chipani cha UTM a Felix Njawala ati
Kusakhidwa kwa a Chakwera ndizakubanja lawo la MCP.

Malingana ndi a Njawala ati “Mungwirizano wa Tonse Alliance pali Dr saulos Chilima
Malingana ndizomwe anthu awiriwa anagwirizana ife sitikututumuka”.

A Njawala anapitilira kunena kuti “Ngwirizano wawo unachitika pamaso pa Khoti
Ndipo ndisindike pano Kuti 2025 Dr Saulos Chilima azapezeka pa Ballot Paper Ngati Mtsogoleri wa Tonse Alliance”.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *