Mpinganjira Walengeza Kuti Athandiza Achinyamata Ndi K18 Million

Wochita malonda Triephornia Mpinganjira walengeza kuti athandiza ndi K18 million achinyamata omwe akufuna kuchita malonda koma alibe kuthekera.

A Mpinganjira alengeza izi pa tsamba lawo la Facebook, ndipo ati iyi ikhala ndalama yothandiza achinyamatawo kuti apeze poyambira.

Kudzera mu ndondomekoyi, wachinyamata aliyense alandira K1 million atapereka pulani yabwino ya malonda omwe akufuna kuchita..

Malinga ndi a Mpinganjira, ndalama yokwana K1 million idzipelekedwa kwa m’nyamata m’modzi pa sabata ziwiri ndipo izi zikhala zikuchitika mpaka mwezi wa December chaka chino.

Achinyamata a zaka za pakati pa 18 ndi 35 ndi omwe akuyenera kutenga nawo gawo pa ndondomeko yomwe akuitcha: “Kuthandiza omwe alibe kuthekela kupita patsogolo”.

Related Posts

Malawi Freedom Network advice President Banda to fight corruption

If you thought Malawians are lazy people, I bet you a Dinosaur, think twice and you will know, check in Read more

David Bisnowaty Israeli-Born Malawi Parliament Member: Actions, Not Words, Will Change Africa for the Better

Malawi MP David Bisnowaty. How does the Israeli-born son of an eastern European Holocaust survivor end up as a parliament Read more

Biography Of Zuneth Sattar

Zuneth Sattar Director of Xaviar Limited and Xaviar Investments Limited Zuneth Sattar is an experienced and knowledgeable property investor. With Read more

Zuneth Sattar Is An Experienced Property Investor

PROPERTY INVESTOR PROPERTY MARKET AN OVERVIEW This blog will cover a wide range of topics and subjects that relate to Sattar’s Read more

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

FDH Launch Islamic Banking Window