“Chinenepetsa nkhumba sichiziwika”: Mustard Gobede wapambana mwa kulima mbewu zosiyanasiyana ndi kuweta nsomba
By Mabvuto Kalawa Pali mwambi wakale woti “chinenepetsa nkhumba sichiziwika,” zomwe zikugwirizana bwino ndi ntchito yolimbika yomwe ikuchitidwa ndi Bambo Mustard Gobede, yemwe ali ndi zaka 45 zakubadwa. Bambo Gobede amachokera m’mudzi…
Read More










