Categories
Sports
Charles Kamanga wachita mutu wa zizwa ndi osewera ake.
Mphunzitsi wamkulu wa timu ya Kamuzu Barracks, Charles Kamanga, wadandaula kuti osewera ake ena akusewera ngati sakufuna. Izi wayankhula kutsatira Kukhadzulidwa 2-0 ndi a nkhondo anzawo kuchokera ku Kaning’ina, Moyale Barracks. Kamanga…
Read More
