Chiwawa pa nkhondo ya ndale ku Nkhotakota: Galimoto ya Grezelda Jeffrey Iphwanyidwa ndi anthu osadziwika
Yolembedwa ndi Burnett Munthali Anthu osadziwika adachita chiwawa pogenda ndi kuswa mazenera a galimoto ya a Grezelda Jeffrey, mmodzi mwa anthu omwe akupikisana pa mpando wa phungu m’dera la Nkhotakota-Chia. Chincident ichi…
Read More










