Kwanu nkwanu mthengo munalaka njoka
Timu ya Premier Bet Dedza Dynamos yalengeza zakubwereranso kuchisa kwa katswiri wa kutsogola, Promise Kamwendo, yemwe anautsa mpungwe-mpungwe pa msika ogula ndi kugulitsa osewera m’dziko muno. Izi zikudza kutsatira chigamulo…