UTM Ikutenga Boma Chaka Cha Mawa-Kaliati

Mlembi wamkuku wa UTM Mayi Kaliati ati UTM ikutenga boma chaka cha mawa.

Iwo ati boma la UTM likubwera kudzakonza chuma komanso kuthana ndi umphawi.Business sector gears up for UTM’s Mega Rally at Masintha Ground

A Kaliati pa msonkhanowu akukamba za momwe chuma cha dziko lino chayendera kuchoka m’zaka za mma 1980 kufika pano, pogwiritsa ntchito mbiri ya chuma yomwe ikuonetsedwa pa kanema wamkuluChrissy Kanyasho Declares Tonse Alliance Defunct; UTM MPs Now in Opposition.

Iwo adzudzula kuyendayenda kunja kwa mtsogoleri wa dziko lino pa nthawi yomwe Amalawi akuvutika ndi umphawi.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *