Mkulu wa malamulo m’dziko muno Thabo Chakaka Nyirenda ali m’dziko la Germany kusaka ndalama za amerika zokwana 543,000 zomwe zidasowa pomwe boma limafuna kugula feteleza
Chakaka Nyirenda wati ali kumeneko kulondoloza mapepala omwe athandizire pa kupezeka kwa ndalamazi
Boma la Malawi linabetsa ndalama zokwana K 750 million ku kampani ya Barkaat Foods Limited yomwe inkati igulitsa unduna wa zaulimi feteleza otsika mtengo
Lowe anatenga ndalama zokwana k30 Billion kupereka ku barkaat foods kuti agule fertilizer ndipo company ya barkaat foods inasowa ndi ndalamazo
Read also: Opposition Wins Election, Ending 58-Year BDP Rule In Botswana
Read also: DPP Vows to Defend Every Vote, Questions MCP’s Use of AI-Generated Results

