Mneneri wachipani cha United Transifomation Movement (UTM) a Felix Njawara watsutsa mphekesera yakuti Ku chipanichi kuli kugawanikana.
Njawala walankhula izi pamsonkhano wa atolankhani womwe chipanichi chikuchititsa mu Mzinda wa Lilongwe.
Mau ake Njawala wati kuchipanichi kulibe kugawanikana kulikonse ndipo Iwo ngati Chipani, amalemekeza malamuro achipanichi motsogozedwa ndi mtsogoleri wawo Dr Michael Usi.
Izi zikudza kutsatira kumangidwa kwa mlembi wa mkulu wa chipanichi Patricia Kaliyati lachinayi sabata ino, yemwe akuganiziridwa kuti amafuna kupalamura mlandu waukulu.
Read also: Ben Longwe reminds Malawians Chakwera’s power ends on 23rd June, 2025
Read also: Bushiri Football Scouting Project Identifies Over 40 Talented Players in Salima
Read also: Deputy Health Minister honors top districts for immunisation efforts

